-
Danieli 2:45Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
45 Zidzachitika mogwirizana ndi zimene munaona kuti mwala unadulidwa kuphiri koma osati ndi manja a munthu ndipo unaphwanya chitsulo, kopa, dongo, siliva ndi golide.+ Inu mfumu, Mulungu Wamkulu wakudziwitsani zimene zidzachitike mʼtsogolo.+ Maloto amenewa adzakwaniritsidwa ndithu ndipo kumasulira kwake nʼkodalirika.”
-