12 Koma pali Ayuda ena amene munawaika kuti aziyangʼanira ntchito za boma mʼchigawo cha Babulo. Amuna amenewa ndi Shadireki, Misheki ndi Abedinego.+ Iwo sakukumverani inu mfumu ndipo sakutumikira milungu yanu moti akukana kulambira fano lagolide limene mwaimika.”