Danieli 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma pali Ayuda ena amene munawaika kukhala oyang’anira chigawo cha Babulo.+ Amuna amphamvu amenewa, Sadirake, Mesake ndi Abedinego, sakukumverani inu mfumu. Iwo sakutumikira milungu yanu ndipo sakulambira fano lagolide limene mwaimika.”+ Danieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:12 Ulosi wa Danieli, ptsa. 74-75
12 Koma pali Ayuda ena amene munawaika kukhala oyang’anira chigawo cha Babulo.+ Amuna amphamvu amenewa, Sadirake, Mesake ndi Abedinego, sakukumverani inu mfumu. Iwo sakutumikira milungu yanu ndipo sakulambira fano lagolide limene mwaimika.”+