Nahumu 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma ngakhale utero, moto udzakuwotcheratu. Lupanga lidzakudula.+ Ndipo lidzakudya ngati mmene dzombe lingʼonolingʼono limadyera zomera.+ Dzichulukitseni ngati dzombe lingʼonolingʼono, Dzichulukitseni ngati dzombe.
15 Koma ngakhale utero, moto udzakuwotcheratu. Lupanga lidzakudula.+ Ndipo lidzakudya ngati mmene dzombe lingʼonolingʼono limadyera zomera.+ Dzichulukitseni ngati dzombe lingʼonolingʼono, Dzichulukitseni ngati dzombe.