Nahumu 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma ngakhale utero, moto udzakunyeketsa. Lupanga lidzakuduladula+ ndipo lidzakudya ngati mmene ana a dzombe oyenda pansi amadyera zomera.+ Dzichulukitseni ngati ana a dzombe oyenda pansi, dzichulukitseni ngati dzombe.
15 Koma ngakhale utero, moto udzakunyeketsa. Lupanga lidzakuduladula+ ndipo lidzakudya ngati mmene ana a dzombe oyenda pansi amadyera zomera.+ Dzichulukitseni ngati ana a dzombe oyenda pansi, dzichulukitseni ngati dzombe.