Zekariya 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti: ‘Ndatsimikiza mtima kuti ndidzateteza Ziyoni.+ Ndatsimikiza kuti ndidzamuteteza nditakwiya kwambiri.’” Zekariya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), ptsa. 2168-2169 Nsanja ya Olonda,1/1/1996, ptsa. 10-11
2 “Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti: ‘Ndatsimikiza mtima kuti ndidzateteza Ziyoni.+ Ndatsimikiza kuti ndidzamuteteza nditakwiya kwambiri.’”