-
Mateyu 8:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Chifukwa inenso ndili ndi akuluakulu ondiyangʼanira komanso ndili ndi asilikali amene ndimawayangʼanira. Ndikauza mmodzi kuti, ‘Pita!’ amapita, wina ndikamuuza kuti, ‘Bwera!’ amabwera. Kapolo wanga ndikamuuza kuti, ‘Chita ichi!’ amachita.”
-