Mateyu 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti inenso ndili ndi akuluakulu ondiyang’anira, komanso ndili ndi asilikali amene ali pansi panga. Ndikauza mmodzi kuti, ‘Pita!’+ amapita, wina ndikamuuza kuti ‘Bwera!’ amabwera. Kapolo wanga ndikamuuza kuti, ‘Chita ichi!’ amachita.”
9 Pakuti inenso ndili ndi akuluakulu ondiyang’anira, komanso ndili ndi asilikali amene ali pansi panga. Ndikauza mmodzi kuti, ‘Pita!’+ amapita, wina ndikamuuza kuti ‘Bwera!’ amabwera. Kapolo wanga ndikamuuza kuti, ‘Chita ichi!’ amachita.”