Mateyu 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako Yesu anauza mtsogoleri wa asilikaliyo kuti: “Pita. Chifukwa chakuti wasonyeza chikhulupiriro, zimene wapemphazo zichitike.”+ Mu ola lomwelo wantchito uja anachira.+
13 Kenako Yesu anauza mtsogoleri wa asilikaliyo kuti: “Pita. Chifukwa chakuti wasonyeza chikhulupiriro, zimene wapemphazo zichitike.”+ Mu ola lomwelo wantchito uja anachira.+