Maliko 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye anawauza kuti: “Musadabwe choncho.+ Ndikudziwa kuti mukufuna Yesu Mnazareti, amene anaphedwa popachikidwa pamtengo. Iyetu waukitsidwa kwa akufa,+ muno mulibe. Taonani, pamene anamugoneka paja si apa!+
6 Iye anawauza kuti: “Musadabwe choncho.+ Ndikudziwa kuti mukufuna Yesu Mnazareti, amene anaphedwa popachikidwa pamtengo. Iyetu waukitsidwa kwa akufa,+ muno mulibe. Taonani, pamene anamugoneka paja si apa!+