Maliko 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye anawauza kuti: “Musadabwe choncho. Ndikudziwa kuti mukufuna Yesu Mnazareti, amene anapachikidwa.+ Iyetu wauka kwa akufa,+ salinso muno ayi. Taonani! Si apa pamene anamugoneka!+
6 Iye anawauza kuti: “Musadabwe choncho. Ndikudziwa kuti mukufuna Yesu Mnazareti, amene anapachikidwa.+ Iyetu wauka kwa akufa,+ salinso muno ayi. Taonani! Si apa pamene anamugoneka!+