Yohane 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Atamaliza kunena zinthu zimenezi, Yesu anatuluka limodzi ndi ophunzira ake nʼkuwoloka chigwa cha Kidironi+ kupita kumene kunali munda. Iye ndi ophunzira akewo analowa mʼmundamo.+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:1 Nsanja ya Olonda,10/1/1990, tsa. 8
18 Atamaliza kunena zinthu zimenezi, Yesu anatuluka limodzi ndi ophunzira ake nʼkuwoloka chigwa cha Kidironi+ kupita kumene kunali munda. Iye ndi ophunzira akewo analowa mʼmundamo.+