Yohane 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Atanena zimenezi, Yesu anatuluka pamodzi ndi ophunzira ake ndi kuwoloka khwawa la Kidironi,+ kupita kumene kunali munda. Ndipo iye ndi ophunzira akewo analowa m’mundamo.+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 18:1 Nsanja ya Olonda,10/1/1990, tsa. 8
18 Atanena zimenezi, Yesu anatuluka pamodzi ndi ophunzira ake ndi kuwoloka khwawa la Kidironi,+ kupita kumene kunali munda. Ndipo iye ndi ophunzira akewo analowa m’mundamo.+