Aefeso 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 anapangitsa kuti tikhale amoyo limodzi ndi Khristu, ngakhale kuti tinali akufa chifukwa cha machimo athu,+ ndipotu inu mwapulumutsidwa chifukwa cha kukoma mtima kwakukulu. Aefeso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:5 Moyo Uno, tsa. 103
5 anapangitsa kuti tikhale amoyo limodzi ndi Khristu, ngakhale kuti tinali akufa chifukwa cha machimo athu,+ ndipotu inu mwapulumutsidwa chifukwa cha kukoma mtima kwakukulu.