15 Ndi thupi lake, anathetsa chinthu choyambitsa chidani, chomwe ndi Chilamulo chimene chinali ndi malamulo komanso malangizo. Anachithetsa kuti magulu awiri omwe ndi ogwirizana ndi iye, akhale munthu mmodzi watsopano+ komanso kuti akhazikitse mtendere.