-
Afilipi 1:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Koma chimene ndikungofuna nʼchakuti makhalidwe anu akhale ogwirizana* ndi uthenga wabwino wa Khristu,+ kuti kaya ndabwera kudzakuonani kapena pamene ine kulibe, ndizimva za inu, kuti mukupitirizabe kukhala ogwirizana.*+ Ndipo ndi mtima umodzi, mukuyesetsa mogwirizana kuti mupitirize kukhulupirira uthenga wabwino.
-