27 Chachikulu, makhalidwe anu akhale oyenera+ uthenga wabwino wa Khristu. Kuti kaya ndabwera kudzakuonani kapena pamene ine kulibe, ndizimva za inu, kuti mukulimbikira mu mzimu umodzi. Ndipo ndi mtima umodzi,+ mukulimbika pamodzi chifukwa cha chikhulupiriro cha uthenga wabwino.