2 Atesalonika 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye amatsutsa komanso kudzikweza pamwamba pa aliyense wotchulidwa kuti mulungu kapena chilichonse chimene chimalambiridwa,* moti amakhala pansi mʼkachisi wa Mulungu nʼkumadzionetsa poyera kuti iye ndi mulungu. 2 Atesalonika Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:4 Nsanja ya Olonda,2/1/1990, ptsa. 11, 13-141/15/1988, tsa. 12
4 Iye amatsutsa komanso kudzikweza pamwamba pa aliyense wotchulidwa kuti mulungu kapena chilichonse chimene chimalambiridwa,* moti amakhala pansi mʼkachisi wa Mulungu nʼkumadzionetsa poyera kuti iye ndi mulungu.