2 Atesalonika 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye ndi wotsutsa+ amene amadzikweza pamwamba pa aliyense wotchedwa “mulungu” kapena chilichonse chopembedzedwa, moti amakhala pansi m’kachisi wa Mulungu, n’kumadzionetsera ngati mulungu.+ 2 Atesalonika Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:4 Nsanja ya Olonda,2/1/1990, ptsa. 11, 13-141/15/1988, tsa. 12
4 Iye ndi wotsutsa+ amene amadzikweza pamwamba pa aliyense wotchedwa “mulungu” kapena chilichonse chopembedzedwa, moti amakhala pansi m’kachisi wa Mulungu, n’kumadzionetsera ngati mulungu.+