-
Aheberi 12:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Tichite zimenezi pamene tikuyangʼanitsitsa Mtumiki Wamkulu ndi Wokwaniritsa chikhulupiriro chathu, Yesu.+ Chifukwa chodziwa kuti adzasangalala mʼtsogolo, anapirira mtengo wozunzikirapo.* Iye sanasamale kuti zochititsa manyazi zimuchitikira ndipo panopa wakhala kudzanja lamanja la mpando wachifumu wa Mulungu.+
-