3 Pogwiritsa ntchito mphamvu yake, Mulungu watipatsa kwaulere zonse zofunikira kuti tikhale ndi moyo komanso kuti tikhale odzipereka kwa iye. Zimenezi zatheka chifukwa chodziwa molondola za Mulungu amene anatiitana+ kudzera mu ulemerero ndi ubwino wake.