2 Petulo 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti Mulungu, mwa mphamvu yake, watipatsa kwaulere zinthu zonse zofunika kuti munthu akhale moyo+ wodzipereka kwa Mulungu.+ Talandira zinthu zimenezi kudzera mwa kudziwa molondola za iye amene anatiitana,+ kudzera mu ulemerero+ ndi ubwino wake. 2 Petulo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:3 Nsanja ya Olonda,9/1/1997, tsa. 103/1/1990, tsa. 13
3 Pakuti Mulungu, mwa mphamvu yake, watipatsa kwaulere zinthu zonse zofunika kuti munthu akhale moyo+ wodzipereka kwa Mulungu.+ Talandira zinthu zimenezi kudzera mwa kudziwa molondola za iye amene anatiitana,+ kudzera mu ulemerero+ ndi ubwino wake.