Chivumbulutso 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako ndinamva mawu kuchokera kumwamba+ akulankhulanso ndi ine kuti: “Pita, katenge mpukutu wotambasula umene uli mʼdzanja la mngelo amene waima panyanja ndi pamtunda uja.”+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:8 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 158-160
8 Kenako ndinamva mawu kuchokera kumwamba+ akulankhulanso ndi ine kuti: “Pita, katenge mpukutu wotambasula umene uli mʼdzanja la mngelo amene waima panyanja ndi pamtunda uja.”+