Chivumbulutso 10:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako, mawu+ amene ndinawamva kuchokera kumwamba aja, analankhulanso ndi ine kuti: “Pita, katenge mpukutu wofunyulula umene uli m’dzanja la mngelo amene waimirira panyanja ndi pamtunda uja.”+ Chivumbulutso Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:8 Mapeto a Chivumbulutso, ptsa. 158-160
8 Kenako, mawu+ amene ndinawamva kuchokera kumwamba aja, analankhulanso ndi ine kuti: “Pita, katenge mpukutu wofunyulula umene uli m’dzanja la mngelo amene waimirira panyanja ndi pamtunda uja.”+