Genesis 41:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Farao atatero, anapatsa Yosefe dzina lakuti, Zafenati-panea.* Anam’patsanso mkazi dzina lake Asenati.+ Mtsikanayu anali mwana wa Potifera, yemwe anali wansembe wa mzinda wa Oni.+ Pamenepo Yosefe anayamba kuyendera dziko la Iguputo.+
45 Farao atatero, anapatsa Yosefe dzina lakuti, Zafenati-panea.* Anam’patsanso mkazi dzina lake Asenati.+ Mtsikanayu anali mwana wa Potifera, yemwe anali wansembe wa mzinda wa Oni.+ Pamenepo Yosefe anayamba kuyendera dziko la Iguputo.+