Genesis 20:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mulungu atandichotsa kunyumba kwa bambo anga+ kuti ndiyambe kuyendayenda, ndinauza mkazi wangayu kuti, ‘Undisonyeze kukoma mtima kosatha+ motere: Kumalo alionse kumene tizifika, uziuza anthu za ine kuti: “Ndi mlongo wanga.”’”+
13 Mulungu atandichotsa kunyumba kwa bambo anga+ kuti ndiyambe kuyendayenda, ndinauza mkazi wangayu kuti, ‘Undisonyeze kukoma mtima kosatha+ motere: Kumalo alionse kumene tizifika, uziuza anthu za ine kuti: “Ndi mlongo wanga.”’”+