Genesis 29:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iye anawafunsanso kuti: “Kodi Labani+ mdzukulu wa Nahori+ mumam’dziwa?” Iwo anati: “Inde timam’dziwa.”
5 Iye anawafunsanso kuti: “Kodi Labani+ mdzukulu wa Nahori+ mumam’dziwa?” Iwo anati: “Inde timam’dziwa.”