Genesis 29:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kenako Labani anafunsa Yakobo kuti: “Kodi ukufuna undigwirire ntchito yaulere+ chifukwa chakuti ndiwe m’bale wanga?+ Ndiuze, kodi ndidzakulipire chiyani?”+ Genesis Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 29:15 Nsanja ya Olonda,10/15/2003, tsa. 29
15 Kenako Labani anafunsa Yakobo kuti: “Kodi ukufuna undigwirire ntchito yaulere+ chifukwa chakuti ndiwe m’bale wanga?+ Ndiuze, kodi ndidzakulipire chiyani?”+