Ekisodo 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Komabe, Farao nayenso anaitana amuna ake anzeru ndi amatsenga.+ Choncho ansembe ochita zamatsenga a ku Iguputo anachitanso zomwezo mwa matsenga awo.+ Ekisodo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:11 Nsanja ya Olonda,1/15/1996, tsa. 24
11 Komabe, Farao nayenso anaitana amuna ake anzeru ndi amatsenga.+ Choncho ansembe ochita zamatsenga a ku Iguputo anachitanso zomwezo mwa matsenga awo.+