Levitiko 4:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 “‘Koma ngati akubweretsa nkhosa+ monga nsembe yake yamachimo, azibweretsa nkhosa yaing’ono yaikazi yopanda chilema.+
32 “‘Koma ngati akubweretsa nkhosa+ monga nsembe yake yamachimo, azibweretsa nkhosa yaing’ono yaikazi yopanda chilema.+