Numeri 20:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 N’chifukwa chiyani munatitulutsa m’dziko la Iguputo kutibweretsa kumalo oipa ano?+ Malo anji osamera mbewu iliyonse? Mitengo ya nkhuyu kulibe kuno, ngakhale mitengo ya mpesa, kapena mitengo ya makangaza.+ Ndi madzi akumwa omwe kulibe!” Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 20:5 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),2/2019, ptsa. 12-13 Nsanja ya Olonda,9/1/2009, tsa. 19
5 N’chifukwa chiyani munatitulutsa m’dziko la Iguputo kutibweretsa kumalo oipa ano?+ Malo anji osamera mbewu iliyonse? Mitengo ya nkhuyu kulibe kuno, ngakhale mitengo ya mpesa, kapena mitengo ya makangaza.+ Ndi madzi akumwa omwe kulibe!”