3 Anakuphunzitsani kudzichepetsa pokukhalitsani ndi njala+ ndi kukudyetsani mana,+ amene inu kapena makolo anu sanawadziwe. Anachita zimenezi kuti mudziwe kuti munthu sakhala ndi moyo ndi chakudya chokha, koma ndi mawu onse ochokera m’kamwa mwa Yehova.+