57 Adzayang’ananso ndi diso loipa zotuluka m’mimba mwake pambuyo pobereka komanso ana ake aamuna amene iye anabereka,+ chifukwa adzawadya mseri pokhala wosowa chilichonse chifukwa cha zovuta ndi nsautso zimene mdani wanu adzakupanikizani nazo m’mizinda yanu.+