24 Anthuwo anamuyankha Yoswa kuti: “Akapolo anufe tinachita zimenezi+ chifukwa tinali ndi mantha aakulu.+ Tinachita mantha titauzidwa mosapita m’mbali za Yehova Mulungu wanu. Tinamva kuti analamula mtumiki wake Mose kuti akupatseni dziko lonse lino, ndi kuti muphe anthu onse okhalamo.+