Oweruza 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Anthu a m’fuko la Zebuloni ndiwo anatonza miyoyo yawo mpaka kuiika pangozi.+Anthu a m’fuko la Nafitali+ nawonso anachita zomwezo m’mapiri a dziko.+
18 Anthu a m’fuko la Zebuloni ndiwo anatonza miyoyo yawo mpaka kuiika pangozi.+Anthu a m’fuko la Nafitali+ nawonso anachita zomwezo m’mapiri a dziko.+