Oweruza 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Komanso ndinakuuzani kuti: “Ine ndine Yehova Mulungu wanu.+ Musaope milungu ya Aamori+ amene mukukhala m’dziko lawo.”+ Koma inu simunamvere mawu anga.’”+
10 Komanso ndinakuuzani kuti: “Ine ndine Yehova Mulungu wanu.+ Musaope milungu ya Aamori+ amene mukukhala m’dziko lawo.”+ Koma inu simunamvere mawu anga.’”+