1 Samueli 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Poyankha anati: “Pitirizani kundikomera mtima ine kapolo wanu.”+ Ndiyeno mkaziyo anachoka ndi kupita kukadya,+ ndipo sanakhalenso ndi nkhawa.+ 1 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:18 Tsanzirani, ptsa. 55-56 Nsanja ya Olonda,7/1/2010, ptsa. 16, 183/15/2007, tsa. 16
18 Poyankha anati: “Pitirizani kundikomera mtima ine kapolo wanu.”+ Ndiyeno mkaziyo anachoka ndi kupita kukadya,+ ndipo sanakhalenso ndi nkhawa.+