-
1 Samueli 14:36Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
36 Kenako Sauli anati: “Tiyeni tipite kwa Afilisiti usiku kuti tikafunkhe zinthu zawo kufikira kutacha,+ ndipo tisasiyepo ngakhale munthu mmodzi pakati pawo.”+ Anthuwo poyankha anati: “Chitani chilichonse chimene mukuona kuti n’chabwino.” Ndiyeno wansembe anati: “Tiyeni tifikire Mulungu woona pamalo ano.”+
-