1 Samueli 14:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Tsopano Sauli anafunsa Yonatani kuti: “Ndiuze, Wachita chiyani?”+ Poyankha, Yonatani anamuuza kuti: “Zoonadi, ndalawa uchi pang’ono kunsonga ya ndodo imene ili m’manja mwangayi.+ Ndiye ndiphenitu!”
43 Tsopano Sauli anafunsa Yonatani kuti: “Ndiuze, Wachita chiyani?”+ Poyankha, Yonatani anamuuza kuti: “Zoonadi, ndalawa uchi pang’ono kunsonga ya ndodo imene ili m’manja mwangayi.+ Ndiye ndiphenitu!”