27 Ndiyeno zimene zinachitika n’zakuti, Davide atangofika ku Mahanaimu, Sobi mwana wamwamuna wa Nahasi, wochokera ku Raba,+ mzinda wa ana a Amoni,+ komanso Makiri+ mwana wa Amiyeli,+ wochokera ku Lo-debara ndi Barizilai+ Mgiliyadi wochokera ku Rogelimu,+