1 Mafumu 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Adalitsike+ Yehova Mulungu wanu, amene wasangalala+ nanu mwa kukuikani pampando wachifumu wa Isiraeli.+ Popeza Yehova adzakonda Isiraeli mpaka kalekale,+ wakuikani kuti mukhale mfumu+ kuti muzipereka zigamulo+ ndi kuchita chilungamo.”+ 1 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:9 Nsanja ya Olonda,11/1/1999, tsa. 20
9 Adalitsike+ Yehova Mulungu wanu, amene wasangalala+ nanu mwa kukuikani pampando wachifumu wa Isiraeli.+ Popeza Yehova adzakonda Isiraeli mpaka kalekale,+ wakuikani kuti mukhale mfumu+ kuti muzipereka zigamulo+ ndi kuchita chilungamo.”+