2 Mafumu 20:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Hezekiya anayankha kuti: “N’zosavuta kuti mthunzi upite kutsogolo masitepe 10, koma osati kubwerera m’mbuyo masitepe 10.”+
10 Hezekiya anayankha kuti: “N’zosavuta kuti mthunzi upite kutsogolo masitepe 10, koma osati kubwerera m’mbuyo masitepe 10.”+