2 Mafumu 23:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Yosiya anachotsanso akachisi onse+ a m’malo okwezeka amene anali m’mizinda+ ya ku Samariya, amene mafumu+ a Isiraeli anamanga kuti akwiyitse Mulungu.+ Iye anawachitira zofanana ndi zonse zimene anachita ku Beteli.+
19 Yosiya anachotsanso akachisi onse+ a m’malo okwezeka amene anali m’mizinda+ ya ku Samariya, amene mafumu+ a Isiraeli anamanga kuti akwiyitse Mulungu.+ Iye anawachitira zofanana ndi zonse zimene anachita ku Beteli.+