2 Mafumu 15:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Izi zinakwaniritsa mawu a Yehova+ amene anawalankhula kwa Yehu, akuti:+ “Ana+ ako aamuna adzakhala pampando wachifumu wa Isiraeli mpaka m’badwo wachinayi.” Ndipo zinaterodi.+
12 Izi zinakwaniritsa mawu a Yehova+ amene anawalankhula kwa Yehu, akuti:+ “Ana+ ako aamuna adzakhala pampando wachifumu wa Isiraeli mpaka m’badwo wachinayi.” Ndipo zinaterodi.+