1 Mbiri 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno Davide anafunsira kwa Mulungu+ kuti: “Kodi ndipite kukamenyana ndi Afilisitiwa? Kodi muwaperekadi m’manja mwanga?” Pamenepo Yehova anauza Davide kuti: “Pita, amenewa ndiwaperekadi m’manja mwako.”
10 Ndiyeno Davide anafunsira kwa Mulungu+ kuti: “Kodi ndipite kukamenyana ndi Afilisitiwa? Kodi muwaperekadi m’manja mwanga?” Pamenepo Yehova anauza Davide kuti: “Pita, amenewa ndiwaperekadi m’manja mwako.”