1 Mbiri 14:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pamenepo Davide anafunsiranso+ kwa Mulungu ndipo Mulungu woonayo anamuyankha kuti: “Ayi usapite kukakumana nawo. Koma uwazembere ndipo ukawaukire kutsogolo kwa zitsamba za baka.*+
14 Pamenepo Davide anafunsiranso+ kwa Mulungu ndipo Mulungu woonayo anamuyankha kuti: “Ayi usapite kukakumana nawo. Koma uwazembere ndipo ukawaukire kutsogolo kwa zitsamba za baka.*+