1 Mbiri 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Matitiya,+ Elifelehu, Mikineya, Obedi-edomu, Yeyeli, ndi Azaziya, anali ndi azeze+ ochunidwa kuti aziimba Seminiti,*+ kuti akhale otsogolera nyimbo. 1 Mbiri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano (nwt), tsa. 2159
21 Matitiya,+ Elifelehu, Mikineya, Obedi-edomu, Yeyeli, ndi Azaziya, anali ndi azeze+ ochunidwa kuti aziimba Seminiti,*+ kuti akhale otsogolera nyimbo.