1 Mbiri 16:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Kenako Davide anasiya Asafu+ ndi abale ake kumeneko pamaso pa likasa la Yehova, kuti azitumikira+ pamaso pa Likasalo nthawi zonse, malinga ndi zofunikira pa tsiku lililonse.+
37 Kenako Davide anasiya Asafu+ ndi abale ake kumeneko pamaso pa likasa la Yehova, kuti azitumikira+ pamaso pa Likasalo nthawi zonse, malinga ndi zofunikira pa tsiku lililonse.+