2 Mbiri 20:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano mzimu+ wa Yehova unafikira Yahazieli yemwe anali pakati pa mpingowo. Iye anali mwana wa Zekariya, Zekariya anali mwana wa Benaya, Benaya anali mwana wa Yeyeli, Yeyeli anali mwana wa Mataniya, Mataniya anali Mlevi, mmodzi wa ana a Asafu.+
14 Tsopano mzimu+ wa Yehova unafikira Yahazieli yemwe anali pakati pa mpingowo. Iye anali mwana wa Zekariya, Zekariya anali mwana wa Benaya, Benaya anali mwana wa Yeyeli, Yeyeli anali mwana wa Mataniya, Mataniya anali Mlevi, mmodzi wa ana a Asafu.+