-
2 Mbiri 25:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Kenako Amaziya anasonkhanitsa Ayuda n’kuwaimiritsa motsatira nyumba ya makolo awo.+ Anawaika m’magulu a anthu 1,000+ ndi mtsogoleri wawo, ndiponso m’magulu a anthu 100+ ndi mtsogoleri wawo, a mafuko a Yuda ndi Benjamini. Iye anawalemba mayina anthuwo, kuyambira azaka 20+ kupita m’tsogolo ndipo anapeza kuti analipo 300,000. Anali amuna ochita kusankhidwa a m’gulu la asilikali, onyamula mkondo waung’ono+ ndi chishango chachikulu.+
-